Snag - Ndidzasekelera Тексты

INTRO
Snag: Though I walk through
the valley of the shadow of
death
Sindidzaopa, popeza ndidziwa
kuti ali nane nthawi zonse. And to all my peoples that
passed
I believe tidzaonananso Yeah VERSE ONE
Snag: Kuli chete, kumidima
mwangoti zii
Kuno kumudzi tingokuwa
misozi
Kodi mwaswela? Mwadzuka? Rest in peace, adzabweranso
wake up
How to address ya, ndachita
jenkha
I dont mind satana ngwa
season Tingodutsa chabe mu his
failing mission
I look upon Jesus I do believe
Ndikhulupira munagonjetsa
imfa
Your prophecies I say Im a believer
Kulira kwa lipenga satana
adzamenya shiver
Tonse kuchitulo
tidzagalamuka
Kumidima kwa satana tidzabalamuka
No more crying and no more
grieving
Celebrating morning,
afternoon, evening
Ayi kulira, ndidzasekelera CHORUS
Refu: I know we gonna meet
one day
Snag: (Rest in peace)
How I wish I could see you
again (Rest in peace)
I miss yall bros
(Rest in peace)
Theres life after death
(Rest in peace) VERSE TWO
Snag: Padziko sikwathu
ndingodutsa kunka kwathu
Balamanthu ndidzatulukira
kwathu
Imfa idzagonja dyabulosi achenjere
Ndzatseka maso kugona
kuusa mumtendere
Inde tikulira koma tikudikilira
Pamene nyengo yakukondwa
idzatifikira Ndzamwemwetera yeah
ndzasekelera
Kuwala mmaso yeah
kudzabwelera
Tsono tigwade pansi tonse
timutame iye Akhale nafe nthawi ndi
nthawi asatisiye
Poti cholengedwa chiri chonse
mwini ndiye
Ife palibe popanda iye
Atate ndipemphera momwe ndinka kukagona
Mwina sindidzuka mawa
sindidzaliona
Mzimu wanga Yesu Khristu
inde mutenge
Ine ndipemphera mzimu wanga muusunge REPEAT CHORUS VERSE THREE
Refu: Limbikani Kaliati,
Trigger (Rest in peace)
Thiya, Mathius Unyolo (Rest in
peace)
Matembo Kumwenda (Rest in peace)
Shobiz, Cosmas Katseka (Rest
in peace)
Tayamba Chatsika (Rest in
peace)
My little bro Twambi(Rest in peace)
Uncle Jeffrey Masamba (Rest
in peace)
Pierre Kwhiliro (Rest in peace)
Rodgers Melssin (Rest in
peace) Mahara Kanyinji (Rest in
peace)
Hard Nock, my DJ Enock
Chibwana (Rest in peace)
Uncle Jo (Rest in peace)
Этот текст прочитали 300 раз.