Nesnes - Wina Watenga Тексты

WINA WATENGA
Nesnes yeah pepa pepa koma wina watenga
Uuuu oh iwe wina watenga pepa pepa

Kusakongola kwanga kuja iwe wina wandikonda
Kupanda ndalama kwanga kuja wina akuti sikupanda chikondi
Chikondi unkandimana chija iwe wina wandipasa
Tsono usandisokonezeso
CHORUS
Iwe wina watenga malo ako baby
Ndati wina watenga chikondi unkachikana chija
Imva wina watenga malo ako baby
Ndati wina watenga pepa pepa

Sataye thawi kundiyimbila moni wako sindiwusowa
Sataye thawi kundiganizila za iwe nayiwala
Chipongwe unkandipanga chija wina akundipasa ulemu
Abale unkawa nyoza aja wina akuwapasa ulemu
Chikondi unachithawa chija iwe wina wachikonda
Ndalimba mtima ine hey
CHORUS
Iwe wina watenga malo ako baby
Ndati wina watenga chikondi ukachikana chija
Imva wina watenga malo ako baby
Ndati wina watenga pepa pepa
Oh oh chikondi cheni cheni ndachipeza ine
Oh oh no sindifuna kubwelelaso mbuyo ine no no
Malo ako wina watenga chikondi unkachiseweresa chija
Iwe wina watenga
Oh oh chikondi cheni cheni ndachipeza ine oh oh
Sindifuna kubwelelaso mbuyo ine yeah
CHORUS
Iwe wina watenga malo ako baby
Ndati wina watenga chikondi ukachikana chija
Imva wina watenga malo ako baby
Ndati wina watenga pepa pepa
Этот текст прочитали 487 раз.